Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 26:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Ndidzathyola kunyada kwanuko, ndi kuchititsa kumwamba kukhala ngati chitsulo+ ndi nthaka yanu ngati mkuwa.

  • Deuteronomo 28:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Thambo limene lili pamwamba pa mutu wako lidzakhala ngati mkuwa, ndipo nthaka yako idzakhala ngati chitsulo.+

  • Yesaya 5:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndidzangousiya kuti uwonongeke.+ Sindidzatengulira mitengo yake ndipo sindidzaulimanso.+ M’mundamo mudzamera tchire ndi zitsamba zaminga,+ ndipo ndidzalamula mitambo kuti isagwetsere mvula pamundawo.+

  • Yeremiya 9:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “Kodi wanzeru ndani kuti amvetse zimenezi, kapenanso ndani amene Yehova wamulankhula kuti anene zimenezi?+ N’chifukwa chiyani dzikoli lidzawonongedwa ndiponso kutenthedwa n’kukhala ngati chipululu chopanda munthu wodutsamo?”+

  • Yeremiya 14:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Alimi achita manyazi moti aphimba mitu yawo chifukwa chakuti m’dzikomo simunagwe mvula+ ndipo nthaka yawonongeka.+

  • Amosi 4:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “‘Ine ndinakumanani mvula kutatsala miyezi itatu kuti mukolole.+ Ndinagwetsa mvula pamzinda umodzi koma pamzinda wina sindinagwetsepo mvula. Mvula inagwa pamunda umodzi koma pamunda wina sindinagwetsepo mvula ndipo unauma.+

  • Hagai 1:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndinalamula kuti chilala chigwe padziko lapansi, pamapiri, pambewu, pavinyo watsopano,+ pamafuta, pazinthu zonse zochokera munthaka, pa anthu, paziweto ndi pa ntchito iliyonse ya manja anu.’”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena