Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Nehemiya 9:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Iwo sanakutumikireni+ ndipo sanabwerere kusiya zoipa zimene anali kuchita+ pamene anali ndi mafumu+ komanso pamene munali kuwapatsa zabwino zochuluka,+ m’dziko lalikulu ndi lachonde+ limene munawapatsa.

  • Yesaya 9:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Anthuwo sanabwerere kwa amene akuwamenya+ ndipo sanafunefune Yehova wa makamu,+

  • Yeremiya 8:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 N’chifukwa chiyani anthu a mu Yerusalemu ali osakhulupirika ndipo akhalabe osakhulupirika kwa nthawi yaitali chonchi? Iwo akupitiriza kuchita zachinyengo+ ndipo akana kubwerera.+

  • Amosi 4:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “‘Komanso ine ndinakupatsani njala*+ m’mizinda yanu yonse ndipo munali kusowa chakudya m’malo anu onse okhala,+ koma simunabwerere kwa ine,’+ watero Yehova.

  • Zekariya 1:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “‘Musakhale ngati makolo anu+ amene aneneri akale anawauza mofuula+ kuti: “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Chonde, siyani njira zanu zoipa ndi zochita zanu zoipa n’kubwerera kwa ine!’”’+

      “‘Koma iwo sanamvere ndipo sanalabadire mawu anga,’+ watero Yehova.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena