Yeremiya 11:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma iwo sanamvere kapena kutchera khutu.+ M’malomwake aliyense wa iwo anapitiriza kuumitsa mtima wake woipawo.+ Choncho ndinawalanga mogwirizana ndi mawu onse amene ndinanena m’pangano langa, amene ndinawalamula kuti awasunge, koma sanawasunge.’” Yeremiya 44:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Ife sitimvera mawu amene watiuza m’dzina la Yehova.+ Zekariya 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma iwo anakanabe kumvetsera.+ Anapitiriza kumulozetsa nkhongo+ ndipo anatseka makutu awo kuti asamve chilichonse.+
8 Koma iwo sanamvere kapena kutchera khutu.+ M’malomwake aliyense wa iwo anapitiriza kuumitsa mtima wake woipawo.+ Choncho ndinawalanga mogwirizana ndi mawu onse amene ndinanena m’pangano langa, amene ndinawalamula kuti awasunge, koma sanawasunge.’”
11 Koma iwo anakanabe kumvetsera.+ Anapitiriza kumulozetsa nkhongo+ ndipo anatseka makutu awo kuti asamve chilichonse.+