Deuteronomo 28:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 chifukwa chakuti sunatumikire Yehova Mulungu wako mokondwera, ndi mtima wosangalala,+ pamene unakhala ndi zochuluka pa chilichonse.+
47 chifukwa chakuti sunatumikire Yehova Mulungu wako mokondwera, ndi mtima wosangalala,+ pamene unakhala ndi zochuluka pa chilichonse.+