Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 12:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Kumalo amenewo, inuyo ndi mabanja anu muzidzadya zimenezi ndi kusangalala ndi zochita zanu zonse+ pamaso pa Yehova,+ chifukwa Yehova Mulungu wanu wakudalitsani.

  • Deuteronomo 32:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Yesuruni*+ atayamba kunenepa, anayamba kupanduka.+

      Iwe wanenepa, wakulupala, wakhuta mopitirira muyezo.+

      Pamenepo iye anasiya Mulungu amene anam’panga,+

      Ndi kunyoza Thanthwe+ la chipulumutso chake.

  • Nehemiya 9:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Iwo sanakutumikireni+ ndipo sanabwerere kusiya zoipa zimene anali kuchita+ pamene anali ndi mafumu+ komanso pamene munali kuwapatsa zabwino zochuluka,+ m’dziko lalikulu ndi lachonde+ limene munawapatsa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena