Zekariya 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako mngelo+ wa Yehova anauza Satana kuti: “Iwe Satana, Yehova akudzudzule!+ Yehova amene anasankha Yerusalemu akudzudzule!+ Kodi munthu uyu si chikuni chimene chaphulidwa pamoto msangamsanga?”+ Yuda 23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Apulumutseni+ mwa kuwakwatula pamoto.+ Pitirizaninso kuchitira chifundo ena onse, koma ndi mantha. Iwo aipitsa zovala zawo zamkati ndi ntchito za thupi. Choncho pamene mukuwachitira chifundo, mutalikirane kwambiri ndi zovala zawo zoipitsidwazo.+
2 Kenako mngelo+ wa Yehova anauza Satana kuti: “Iwe Satana, Yehova akudzudzule!+ Yehova amene anasankha Yerusalemu akudzudzule!+ Kodi munthu uyu si chikuni chimene chaphulidwa pamoto msangamsanga?”+
23 Apulumutseni+ mwa kuwakwatula pamoto.+ Pitirizaninso kuchitira chifundo ena onse, koma ndi mantha. Iwo aipitsa zovala zawo zamkati ndi ntchito za thupi. Choncho pamene mukuwachitira chifundo, mutalikirane kwambiri ndi zovala zawo zoipitsidwazo.+