Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 7:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Kenako iye anapanga thanki yamkuwa.*+ Pakamwa pa thankiyo panali papakulu mikono 10 kuyeza modutsa pakati pake, ndipo panali pozungulira. Thankiyo inali yaitali mikono isanu kuchokera pansi kufika pamwamba. Pankafunika chingwe chotalika mikono 30 kuti ayeze kuzungulira thankiyo.+

  • 1 Mafumu 7:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Anaika zotengera zisanu mbali ya kudzanja lamanja kwa nyumbayo ndi zotengera zina zisanu mbali ya kumanzere kwa nyumbayo.+ Thanki ija anaiika mbali ya kudzanja lamanja kwa nyumbayo, kum’mawa chakum’mwera kwake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena