1 Yohane 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Tikudziwa kuti munthu aliyense amene ali mwana wa Mulungu+ sakhala ndi chizolowezi chochita tchimo, koma mwana*+ wa Mulungu amamuyang’anira, ndipo woipayo samugwira.+
18 Tikudziwa kuti munthu aliyense amene ali mwana wa Mulungu+ sakhala ndi chizolowezi chochita tchimo, koma mwana*+ wa Mulungu amamuyang’anira, ndipo woipayo samugwira.+