1 Yohane 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Onse amene amakhulupirira kuti Yesu ndi Khristu, ndi ana a Mulungu,+ ndipo onse amene amakonda Atate amakondanso mwana wake.+
5 Onse amene amakhulupirira kuti Yesu ndi Khristu, ndi ana a Mulungu,+ ndipo onse amene amakonda Atate amakondanso mwana wake.+