Yohane 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Zinthu zonse zimene Atate ali nazo ndi zanga.+ Nʼchifukwa chake ndikunena kuti mthandiziyo adzalengeza kwa inu zinthu zimene walandira kuchokera kwa ine.
15 Zinthu zonse zimene Atate ali nazo ndi zanga.+ Nʼchifukwa chake ndikunena kuti mthandiziyo adzalengeza kwa inu zinthu zimene walandira kuchokera kwa ine.