Genesis 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndidzaika+ chidani+ pakati pa iwe+ ndi mkaziyo,+ ndi pakati pa mbewu yako+ ndi mbewu yake.+ Mbewu ya mkaziyo+ idzaphwanya mutu wako,+ ndipo iwe+ udzaivulaza chidendene.”+ Luka 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno iye anawauza kuti: “Ndinayamba kuona Satana atagwa+ kale ngati mphezi kuchokera kumwamba. 1 Yohane 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Amene amachitabe tchimo anachokera kwa Mdyerekezi, chifukwa Mdyerekezi wakhala akuchimwa kuyambira pa chiyambi.+ Choncho, Mwana wa Mulungu anaonekera+ kuti awononge ntchito za Mdyerekezi.+
15 Ndidzaika+ chidani+ pakati pa iwe+ ndi mkaziyo,+ ndi pakati pa mbewu yako+ ndi mbewu yake.+ Mbewu ya mkaziyo+ idzaphwanya mutu wako,+ ndipo iwe+ udzaivulaza chidendene.”+
8 Amene amachitabe tchimo anachokera kwa Mdyerekezi, chifukwa Mdyerekezi wakhala akuchimwa kuyambira pa chiyambi.+ Choncho, Mwana wa Mulungu anaonekera+ kuti awononge ntchito za Mdyerekezi.+