Yesaya 54:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Pakuti Wokupanga Wamkulu+ ndiye mwamuna wako.+ Dzina lake ndi Yehova wa makamu,+ ndipo Woyera wa Isiraeli ndiye Wokuwombola.+ Iye adzatchedwa Mulungu wa dziko lonse lapansi.+ Agalatiya 4:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma Yerusalemu+ wam’mwamba ndi mfulu, ndipo ndiye mayi wathu.+ Chivumbulutso 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako chizindikiro chachikulu+ chinaoneka kumwamba. Ndicho mkazi+ atavala dzuwa, ndipo mwezi unali kunsi kwa mapazi ake. Kumutu kwake kunali chisoti chachifumu chokhala ndi nyenyezi 12,
5 “Pakuti Wokupanga Wamkulu+ ndiye mwamuna wako.+ Dzina lake ndi Yehova wa makamu,+ ndipo Woyera wa Isiraeli ndiye Wokuwombola.+ Iye adzatchedwa Mulungu wa dziko lonse lapansi.+
12 Kenako chizindikiro chachikulu+ chinaoneka kumwamba. Ndicho mkazi+ atavala dzuwa, ndipo mwezi unali kunsi kwa mapazi ake. Kumutu kwake kunali chisoti chachifumu chokhala ndi nyenyezi 12,