Yesaya 48:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti iwo amadzitcha kuti amakhala mumzinda woyera,+ ndipo amadalira Mulungu wa Isiraeli+ amene dzina lake ndi Yehova wa makamu.+ Yeremiya 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma Mulungu wa Yakobo+ sali ngati mafanowa. Iye ndi amene anapanga china chilichonse.+ Isiraeli ndiye ndodo ya cholowa chake.+ Dzina la Mulunguyo ndi Yehova wa makamu.+
2 Pakuti iwo amadzitcha kuti amakhala mumzinda woyera,+ ndipo amadalira Mulungu wa Isiraeli+ amene dzina lake ndi Yehova wa makamu.+
16 Koma Mulungu wa Yakobo+ sali ngati mafanowa. Iye ndi amene anapanga china chilichonse.+ Isiraeli ndiye ndodo ya cholowa chake.+ Dzina la Mulunguyo ndi Yehova wa makamu.+