Yeremiya 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma Mulungu, amene ndi cholowa cha Yakobo, sali ngati mafano amenewa,Chifukwa iye ndi amene anapanga china chilichonse,Ndipo Isiraeli ndi ndodo ya cholowa chake.+ Dzina lake ndi Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.+
16 Koma Mulungu, amene ndi cholowa cha Yakobo, sali ngati mafano amenewa,Chifukwa iye ndi amene anapanga china chilichonse,Ndipo Isiraeli ndi ndodo ya cholowa chake.+ Dzina lake ndi Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.+