Yesaya 47:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Pali amene akutiwombola.+ Dzina lake ndi Yehova wa makamu,+ Woyera wa Isiraeli.”+ Yeremiya 51:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Koma Mulungu wa Yakobo sali ngati mafanowa.+ Iye ndi amene anapanga china chilichonse.+ Mulungu ameneyu ndiye ndodo ya cholowa chake+ ndipo dzina lake ndi Yehova wa makamu.”+
19 “Koma Mulungu wa Yakobo sali ngati mafanowa.+ Iye ndi amene anapanga china chilichonse.+ Mulungu ameneyu ndiye ndodo ya cholowa chake+ ndipo dzina lake ndi Yehova wa makamu.”+