Mika 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Iwe mzinda wogonjetsedwa, tsopano udzichekecheke.+ Adani atizungulira kuti atiukire.+ Iwo adzamenya woweruza wa Isiraeli patsaya ndi ndodo.+ Mateyu 27:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Pamenepo Yesu anafuulanso mokweza mawu, kenako anatsirizika.+ Machitidwe 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chotero munapha Mtumiki Wamkulu wa moyo,+ koma Mulungu anamuukitsa kwa akufa, ndipo ife ndife mboni za choonadi chimenechi.+ Afilipi 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kuposanso pamenepo, atakhala munthu,+ anadzichepetsa ndi kukhala womvera mpaka imfa.+ Anakhala womvera mpaka imfa ya pamtengo wozunzikirapo.*+
5 “Iwe mzinda wogonjetsedwa, tsopano udzichekecheke.+ Adani atizungulira kuti atiukire.+ Iwo adzamenya woweruza wa Isiraeli patsaya ndi ndodo.+
15 Chotero munapha Mtumiki Wamkulu wa moyo,+ koma Mulungu anamuukitsa kwa akufa, ndipo ife ndife mboni za choonadi chimenechi.+
8 Kuposanso pamenepo, atakhala munthu,+ anadzichepetsa ndi kukhala womvera mpaka imfa.+ Anakhala womvera mpaka imfa ya pamtengo wozunzikirapo.*+