Yesaya 35:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Amene ali ndi nkhawa mumtima mwawo muwauze kuti:+ “Limbani mtima.+ Musachite mantha.+ Pakuti Mulungu wanu adzabwera n’kudzabwezera adani anu.+ Mulungu adzabwezera chilango.+ Iye adzabwera n’kukupulumutsani.”+ Yesaya 43:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ine ndine Yehova.+ Popanda ine palibenso mpulumutsi wina.”+ Aheberi 10:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kulandira chilango chochokera kwa Mulungu wamoyo n’chinthu choopsa.+
4 Amene ali ndi nkhawa mumtima mwawo muwauze kuti:+ “Limbani mtima.+ Musachite mantha.+ Pakuti Mulungu wanu adzabwera n’kudzabwezera adani anu.+ Mulungu adzabwezera chilango.+ Iye adzabwera n’kukupulumutsani.”+