Salimo 56:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ine ndidzadalira inu, tsiku lililonse limene ndingachite mantha.+ Zefaniya 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsiku limenelo Yerusalemu adzauzidwa kuti: “Usaope iwe Ziyoni+ ndipo usalefuke.+ Mateyu 10:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Musachite mantha+ ndi amene amapha thupi koma sangaphe moyo, m’malomwake, muziopa iye+ amene angathe kuwononga zonse ziwiri, moyo ndi thupi lomwe m’Gehena.*+ Aheberi 10:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 “Koma wolungama wanga adzakhala ndi moyo mwa chikhulupiriro chake,”+ ndipo “ngati wabwerera m’mbuyo, ine sindikondwera naye.”+
28 Musachite mantha+ ndi amene amapha thupi koma sangaphe moyo, m’malomwake, muziopa iye+ amene angathe kuwononga zonse ziwiri, moyo ndi thupi lomwe m’Gehena.*+
38 “Koma wolungama wanga adzakhala ndi moyo mwa chikhulupiriro chake,”+ ndipo “ngati wabwerera m’mbuyo, ine sindikondwera naye.”+