Miyambo 12:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Nkhawa mumtima mwa munthu ndi imene imauweramitsa,+ koma mawu abwino ndi amene amausangalatsa.+