Yeremiya 51:56 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Wofunkha adzafikira Babulo+ ndipo amuna ake amphamvu adzagwidwa.+ Mauta awo adzathyoledwa,+ pakuti Yehova ndi Mulungu wobwezera.+ Iye adzawabwezera ndithu.+ 2 Atesalonika 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chiweruzo cha Mulunguchi n’cholungama chifukwa akubwezera masautso kwa amene amakusautsani.+ Chivumbulutso 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo anafuula ndi mawu okweza akuti: “Mudzalekerera kufikira liti, Inu Ambuye Wamkulu Koposa,+ woyera ndi woona,+ osaweruza+ ndi kubwezera okhala padziko lapansi chifukwa cha magazi+ athu?”
56 Wofunkha adzafikira Babulo+ ndipo amuna ake amphamvu adzagwidwa.+ Mauta awo adzathyoledwa,+ pakuti Yehova ndi Mulungu wobwezera.+ Iye adzawabwezera ndithu.+
10 Iwo anafuula ndi mawu okweza akuti: “Mudzalekerera kufikira liti, Inu Ambuye Wamkulu Koposa,+ woyera ndi woona,+ osaweruza+ ndi kubwezera okhala padziko lapansi chifukwa cha magazi+ athu?”