Yeremiya 50:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Lupanga lidzawononga anthu olankhula zinthu zopanda pake.+ Anthu amenewo adzachita zinthu mopanda nzeru.+ Lupanga lidzawononga anthu amphamvu a m’Babulo,+ moti adzagwidwa ndi mantha.+
36 Lupanga lidzawononga anthu olankhula zinthu zopanda pake.+ Anthu amenewo adzachita zinthu mopanda nzeru.+ Lupanga lidzawononga anthu amphamvu a m’Babulo,+ moti adzagwidwa ndi mantha.+