-
Yeremiya 51:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Kudzera mwa iwe ndidzaphwanya m’busa ndi gulu lake la ziweto kukhala zidutswazidutswa. Kudzera mwa iwe ndidzaphwanya mlimi ndi ziweto zake zolimira kukhala zidutswazidutswa. Kudzera mwa iwe ndidzaphwanya abwanamkubwa ndi atsogoleri kukhala zidutswazidutswa.
-