Yesaya 44:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndimalepheretsa zizindikiro za anthu olankhula zinthu zopanda pake, ndipo ndine amene ndimachititsa olosera kuchita zamisala.+ Ndine amene ndimachititsa anthu anzeru kubwerera kumbuyo, ndiponso amene ndimachititsa nzeru zawo kukhala zopusa.+
25 Ndimalepheretsa zizindikiro za anthu olankhula zinthu zopanda pake, ndipo ndine amene ndimachititsa olosera kuchita zamisala.+ Ndine amene ndimachititsa anthu anzeru kubwerera kumbuyo, ndiponso amene ndimachititsa nzeru zawo kukhala zopusa.+