2 Samueli 15:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kenako uthenga unafika kwa Davide wonena kuti: “Ahitofeli nayenso ali pakati pa anthu amene akukonza chiwembu+ pamodzi ndi Abisalomu.”+ Pamenepo Davide anati:+ “Inu Yehova!+ Chonde, sandutsani malangizo a Ahitofeli kuti akhale opusa.”+ Yesaya 29:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 ine ndidzachitanso zodabwitsa ndi anthu awa.+ Ndidzazichita m’njira yodabwitsa, pogwiritsira ntchito chinthu chodabwitsa. Nzeru za anthu awo anzeru zidzatha, ndipo kumvetsetsa zinthu kwa anthu awo ozindikira kudzabisika.”+ 1 Akorinto 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pakuti Malemba amati: “Ndidzathetsa nzeru zonse za anthu anzeru,+ ndipo ndidzakankhira pambali+ kuchenjera kwa anthu ophunzira.”+
31 Kenako uthenga unafika kwa Davide wonena kuti: “Ahitofeli nayenso ali pakati pa anthu amene akukonza chiwembu+ pamodzi ndi Abisalomu.”+ Pamenepo Davide anati:+ “Inu Yehova!+ Chonde, sandutsani malangizo a Ahitofeli kuti akhale opusa.”+
14 ine ndidzachitanso zodabwitsa ndi anthu awa.+ Ndidzazichita m’njira yodabwitsa, pogwiritsira ntchito chinthu chodabwitsa. Nzeru za anthu awo anzeru zidzatha, ndipo kumvetsetsa zinthu kwa anthu awo ozindikira kudzabisika.”+
19 Pakuti Malemba amati: “Ndidzathetsa nzeru zonse za anthu anzeru,+ ndipo ndidzakankhira pambali+ kuchenjera kwa anthu ophunzira.”+