Yesaya 28:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yehova adzaimirira monga mmene anachitira paphiri la Perazimu.+ Adzakalipa ngati mmene anachitira m’chigwa cha kufupi ndi Gibeoni+ kuti achite ntchito yake. Ntchito yakeyo ndi yodabwitsa. Adzakalipa kuti achite zochita zake. Zochita zakezo n’zachilendo.+ Habakuku 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Yang’anani pakati pa mitundu ya anthu ena anthu inu, ndipo muyang’anitsitse, kenako muyang’anane modabwa.+ Dabwani pakuti pali ntchito imene winawake akuichita m’masiku anu imene anthu inu simungakhulupirire ngakhale wina atakufotokozerani.+
21 Yehova adzaimirira monga mmene anachitira paphiri la Perazimu.+ Adzakalipa ngati mmene anachitira m’chigwa cha kufupi ndi Gibeoni+ kuti achite ntchito yake. Ntchito yakeyo ndi yodabwitsa. Adzakalipa kuti achite zochita zake. Zochita zakezo n’zachilendo.+
5 “Yang’anani pakati pa mitundu ya anthu ena anthu inu, ndipo muyang’anitsitse, kenako muyang’anane modabwa.+ Dabwani pakuti pali ntchito imene winawake akuichita m’masiku anu imene anthu inu simungakhulupirire ngakhale wina atakufotokozerani.+