Yesaya 28:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yehova adzaimirira ngati mmene anachitira paphiri la Perazimu.Adzaimirira ngati mmene anachitira mʼchigwa, pafupi ndi Gibiyoni,+Kuti achite zochita zake, zochita zake zodabwitsa,Komanso kuti agwire ntchito yake, ntchito yake yachilendo.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:21 Yesaya 1, tsa. 295 Nsanja ya Olonda,6/1/1991, ptsa. 20-25
21 Yehova adzaimirira ngati mmene anachitira paphiri la Perazimu.Adzaimirira ngati mmene anachitira mʼchigwa, pafupi ndi Gibiyoni,+Kuti achite zochita zake, zochita zake zodabwitsa,Komanso kuti agwire ntchito yake, ntchito yake yachilendo.+