Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 41:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Koma munthu amene ndinali kukhala naye mwamtendere, amene ndinali kumukhulupirira,+

      Munthu amene anali kudya chakudya changa,+ wakweza chidendene chake kundiukira.+

  • Salimo 55:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pakuti amene ananditonza si mdani.+

      Akanakhala mdani ndikanapirira.

      Amene anadzikweza pamaso panga si munthu wodana nane kwambiri.+

      Akanakhala munthu wodana nane kwambiri ndikanabisala.+

  • Mateyu 26:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 n’kuwafunsa kuti: “Kodi mudzandipatsa chiyani ndikamupereka kwa inu?”+ Iwo anamulonjeza ndalama 30 zasiliva.+

  • Yohane 13:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Sindikunena nonsenu, ndikudziwa amene ndawasankha.+ Koma zili choncho kuti Malemba akwaniritsidwe,+ paja amati, ‘Munthu amene anali kudya chakudya changa wanyamula chidendene chake kundiukira.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena