Salimo 41:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma munthu amene ndinali kukhala naye mwamtendere, amene ndinali kumukhulupirira,+Munthu amene anali kudya chakudya changa,+ wakweza chidendene chake kundiukira.+ Mateyu 26:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Poyankha iye anati: “Amene akusunsa nane limodzi m’mbalemu ndi amene ati andipereke.+
9 Koma munthu amene ndinali kukhala naye mwamtendere, amene ndinali kumukhulupirira,+Munthu amene anali kudya chakudya changa,+ wakweza chidendene chake kundiukira.+