Obadiya 7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu onse amene unachita nawo pangano akupusitsa+ ndipo akuthamangitsira kumalire. Anthu amene unali kukhala nawo mwamtendere akugonjetsa.+ Anthu amene ukudya nawo limodzi adzakutchera ukonde, ndipo udzakhala ngati munthu wosazindikira.+
7 Anthu onse amene unachita nawo pangano akupusitsa+ ndipo akuthamangitsira kumalire. Anthu amene unali kukhala nawo mwamtendere akugonjetsa.+ Anthu amene ukudya nawo limodzi adzakutchera ukonde, ndipo udzakhala ngati munthu wosazindikira.+