Obadiya 7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu amene unachita nawo mgwirizano* akuthamangitsira kumalire. Onsewo akupusitsa. Anthu amene unkakhala nawo mwamtendere akugonjetsa. Anthu amene ukudya nawo limodzi adzakutchera ukonde,Koma iwe sudzazindikira.” Obadiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7 Tsiku la Yehova, ptsa. 135-136 Nsanja ya Olonda,4/15/1989, tsa. 30
7 Anthu amene unachita nawo mgwirizano* akuthamangitsira kumalire. Onsewo akupusitsa. Anthu amene unkakhala nawo mwamtendere akugonjetsa. Anthu amene ukudya nawo limodzi adzakutchera ukonde,Koma iwe sudzazindikira.”