Maliko 14:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndipo akudya chakudya patebulo, Yesu anati: “Ndithu ndikukuuzani, Mmodzi wa inu, amene akudya+ nane limodzi, andipereka.”+ Yohane 13:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Sindikunena nonsenu, ndikudziwa amene ndawasankha.+ Koma zili choncho kuti Malemba akwaniritsidwe,+ paja amati, ‘Munthu amene anali kudya chakudya changa wanyamula chidendene chake kundiukira.’+ Yohane 13:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Yesu anayankha kuti: “Ndi amene ndimupatse chidutswa cha mkate chimene ndisunse.”+ Choncho atasunsa chidutswa cha mkate chija, anapatsa Yudasi, mwana wa Simoni Isikariyoti.
18 Ndipo akudya chakudya patebulo, Yesu anati: “Ndithu ndikukuuzani, Mmodzi wa inu, amene akudya+ nane limodzi, andipereka.”+
18 Sindikunena nonsenu, ndikudziwa amene ndawasankha.+ Koma zili choncho kuti Malemba akwaniritsidwe,+ paja amati, ‘Munthu amene anali kudya chakudya changa wanyamula chidendene chake kundiukira.’+
26 Yesu anayankha kuti: “Ndi amene ndimupatse chidutswa cha mkate chimene ndisunse.”+ Choncho atasunsa chidutswa cha mkate chija, anapatsa Yudasi, mwana wa Simoni Isikariyoti.