Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 21:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Ngati yagunda kapolo wamwamuna kapena wamkazi, mwiniwake azilipira ndalama zokwana masekeli* 30+ kwa mbuye wa kapoloyo, ndipo ng’ombeyo iziponyedwa miyala.

  • Zekariya 11:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Kenako ndinawauza kuti: “Ngati mukuona kuti n’zoyenera,+ ndipatseni malipiro anga, koma ngati mukuona kuti n’zosayenera musandipatse.” Pamenepo iwo anandipatsa ndalama 30 zasiliva monga malipiro anga.+

  • Mateyu 27:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pamenepo Yudasi amene anam’pereka uja ataona kuti Yesu waweruzidwa kuti aphedwe, anavutika koopsa mumtima mwake moti anapita kukabweza ndalama 30+ zasiliva zija kwa ansembe aakulu ndiponso akulu.

  • Maliko 14:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Atamva zimenezo, iwo anasangalala ndi kumulonjeza kuti am’patsa ndalama zasiliva.+ Choncho iye anayamba kufunafuna mpata wabwino umene angamuperekere.+

  • Luka 22:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Iwo anakondwa, ndipo anagwirizana kuti amupatse ndalama zasiliva.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena