Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 8:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Anthu anzeru achita manyazi.+ Achita mantha ndipo adzagwidwa. Taonani! Iwo akana mawu a Yehova. Kodi ali ndi nzeru yotani tsopano?+

  • Yohane 9:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Ndiyeno Yesu ananena kuti: “Ndinabwera m’dziko lino kudzapereka chiweruzo ichi:+ Osaona ayambe kuona,+ ndipo oona akhale akhungu.”+

  • Machitidwe 28:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Mzimuwo unati, ‘Pita ukauze anthu awa kuti: “Kumva mudzamva ndithu, koma osazindikira ngakhale pang’ono. Kupenya mudzapenya ndithu, koma osaona ngakhale pang’ono.+

  • Aroma 1:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Ndiponso monga mmene iwo sanafunire kumudziwa Mulungu molondola,+ iye anawasiya ndi maganizo awo oipa,+ kuti azichita zinthu zosayenerazo,+

  • 1 Akorinto 1:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Pakuti Malemba amati: “Ndidzathetsa nzeru zonse za anthu anzeru,+ ndipo ndidzakankhira pambali+ kuchenjera kwa anthu ophunzira.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena