Levitiko 26:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Motero ndidzayendadi pakati panu ndi kukusonyezani kuti ine ndine Mulungu wanu,+ ndipo inu mudzakhala anthu anga.+ Ezekieli 37:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Iwo adzakhala muhema wanga.+ Ine ndidzakhaladi Mulungu wawo ndipo iwo adzakhala anthu anga.+ Zekariya 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndithu ndidzawabweretsa, ndipo adzakhala mu Yerusalemu.+ Iwo adzakhala anthu anga+ ndipo ine ndidzakhala Mulungu wawo woona ndi wachilungamo.’”+
12 Motero ndidzayendadi pakati panu ndi kukusonyezani kuti ine ndine Mulungu wanu,+ ndipo inu mudzakhala anthu anga.+
8 Ndithu ndidzawabweretsa, ndipo adzakhala mu Yerusalemu.+ Iwo adzakhala anthu anga+ ndipo ine ndidzakhala Mulungu wawo woona ndi wachilungamo.’”+