Ekisodo 29:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Choncho ndidzakhala pakati pa ana a Isiraeli, ndipo ndidzakhala Mulungu wawo.+ Levitiko 26:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ine ndidzaika chihema changa chopatulika pakati panu,+ ndipo sindidzanyansidwa nanu.+