Salimo 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu Yehova Ambuye wathu, dzina lanu ndi lalikulu padziko lonse lapansi,+Inuyo ulemerero wanu ukusimbidwa kumwambamwamba!+ Salimo 83:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kuti anthu adziwe+ kuti inu, amene dzina lanu ndinu Yehova,+Inu nokha ndinu Wam’mwambamwamba,+ wolamulira dziko lonse lapansi.+ Hoseya 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye ndi Yehova Mulungu wa makamu.+ Yehova ndilo dzina lake lomukumbukira nalo.+
8 Inu Yehova Ambuye wathu, dzina lanu ndi lalikulu padziko lonse lapansi,+Inuyo ulemerero wanu ukusimbidwa kumwambamwamba!+
18 Kuti anthu adziwe+ kuti inu, amene dzina lanu ndinu Yehova,+Inu nokha ndinu Wam’mwambamwamba,+ wolamulira dziko lonse lapansi.+