Salimo 37:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Woipa amalondalonda munthu wolungama,+Ndipo amafuna kuti amuphe.+ Mateyu 14:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Komabe, ngakhale kuti Herode ankafuna kupha Yohane, anaopa khamu la anthu, chifukwa iwo anali kukhulupirira kuti ndi mneneri.+
5 Komabe, ngakhale kuti Herode ankafuna kupha Yohane, anaopa khamu la anthu, chifukwa iwo anali kukhulupirira kuti ndi mneneri.+