Mateyu 21:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Komanso sitinganene kuti, ‘Unachokera kwa anthu,’ chifukwa tikuopa khamu la anthuli,+ pakuti onsewa amakhulupirira kuti Yohane anali mneneri.”+ Maliko 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Herode anali kulemekeza+ Yohane, pakuti anali kumudziwa kuti ndi munthu wolungama ndi woyera,+ choncho anali kumusunga bwino. Atamva+ zonena zake anathedwa nzeru, komabe anapitiriza kumumvetsera mokondwa. Luka 1:76 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 76 Koma kunena za iwe, mwanawe, udzatchedwa mneneri wa Wam’mwambamwamba, pakuti udzatsogola pamaso pa Yehova kuti ukakonzeretu njira zake.+ Luka 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma tikanena kuti, ‘Unachokera kwa anthu,’ anthu onsewa atiponya miyala,+ chifukwa iwo akukhulupirira ndi mtima wonse kuti Yohane+ anali mneneri.”+
26 Komanso sitinganene kuti, ‘Unachokera kwa anthu,’ chifukwa tikuopa khamu la anthuli,+ pakuti onsewa amakhulupirira kuti Yohane anali mneneri.”+
20 Herode anali kulemekeza+ Yohane, pakuti anali kumudziwa kuti ndi munthu wolungama ndi woyera,+ choncho anali kumusunga bwino. Atamva+ zonena zake anathedwa nzeru, komabe anapitiriza kumumvetsera mokondwa.
76 Koma kunena za iwe, mwanawe, udzatchedwa mneneri wa Wam’mwambamwamba, pakuti udzatsogola pamaso pa Yehova kuti ukakonzeretu njira zake.+
6 Koma tikanena kuti, ‘Unachokera kwa anthu,’ anthu onsewa atiponya miyala,+ chifukwa iwo akukhulupirira ndi mtima wonse kuti Yohane+ anali mneneri.”+