Machitidwe 24:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Patapita masiku angapo, Felike+ anafika pamodzi ndi mkazi wake Durusila, amene anali mayi wachiyuda.+ Choncho Felike anaitanitsa Paulo ndi kumumvetsera pamene anali kufotokoza za kukhulupirira Khristu Yesu.+
24 Patapita masiku angapo, Felike+ anafika pamodzi ndi mkazi wake Durusila, amene anali mayi wachiyuda.+ Choncho Felike anaitanitsa Paulo ndi kumumvetsera pamene anali kufotokoza za kukhulupirira Khristu Yesu.+