Mateyu 21:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Komanso sitinganene kuti, ‘Unachokera kwa anthu,’ chifukwa tikuopa khamu la anthuli,+ pakuti onsewa amakhulupirira kuti Yohane anali mneneri.”+
26 Komanso sitinganene kuti, ‘Unachokera kwa anthu,’ chifukwa tikuopa khamu la anthuli,+ pakuti onsewa amakhulupirira kuti Yohane anali mneneri.”+