Mateyu 14:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Komabe, ngakhale kuti Herode ankafuna kupha Yohane, anaopa khamu la anthu, chifukwa iwo anali kukhulupirira kuti ndi mneneri.+ Mateyu 21:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Komabe, ngakhale kuti anali kufunafuna mpata wakuti amugwire, ankaopa khamu la anthu, chifukwa anthuwo anali kukhulupirira kuti iye ndi mneneri.+
5 Komabe, ngakhale kuti Herode ankafuna kupha Yohane, anaopa khamu la anthu, chifukwa iwo anali kukhulupirira kuti ndi mneneri.+
46 Komabe, ngakhale kuti anali kufunafuna mpata wakuti amugwire, ankaopa khamu la anthu, chifukwa anthuwo anali kukhulupirira kuti iye ndi mneneri.+