Maliko 11:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Koma nanga tinganene kuti ‘Unachokera kwa anthu’ ngati?” . . . Anali kuopa khamu la anthu, chifukwa anthu onsewo anali kukhulupirira kuti Yohane analidi mneneri.+ Luka 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma tikanena kuti, ‘Unachokera kwa anthu,’ anthu onsewa atiponya miyala,+ chifukwa iwo akukhulupirira ndi mtima wonse kuti Yohane+ anali mneneri.”+
32 Koma nanga tinganene kuti ‘Unachokera kwa anthu’ ngati?” . . . Anali kuopa khamu la anthu, chifukwa anthu onsewo anali kukhulupirira kuti Yohane analidi mneneri.+
6 Koma tikanena kuti, ‘Unachokera kwa anthu,’ anthu onsewa atiponya miyala,+ chifukwa iwo akukhulupirira ndi mtima wonse kuti Yohane+ anali mneneri.”+