Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 3:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Choncho anthu ochokera ku Yerusalemu ndi ku Yudeya konse ndiponso ochokera m’midzi yonse yapafupi ndi Yorodano anali kubwera kwa iye.

  • Mateyu 14:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Komabe, ngakhale kuti Herode ankafuna kupha Yohane, anaopa khamu la anthu, chifukwa iwo anali kukhulupirira kuti ndi mneneri.+

  • Mateyu 21:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Komanso sitinganene kuti, ‘Unachokera kwa anthu,’ chifukwa tikuopa khamu la anthuli,+ pakuti onsewa amakhulupirira kuti Yohane anali mneneri.”+

  • Maliko 6:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Herode anali kulemekeza+ Yohane, pakuti anali kumudziwa kuti ndi munthu wolungama ndi woyera,+ choncho anali kumusunga bwino. Atamva+ zonena zake anathedwa nzeru, komabe anapitiriza kumumvetsera mokondwa.

  • Luka 20:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Koma tikanena kuti, ‘Unachokera kwa anthu,’ anthu onsewa atiponya miyala,+ chifukwa iwo akukhulupirira ndi mtima wonse kuti Yohane+ anali mneneri.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena