Salimo 17:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano adaniwo atizungulira, kulikonse kumene tingapite.+Akutiyang’anitsitsa kuti atigwetse.+ Yeremiya 22:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 ‘Ndithudi, maso ako ndi mtima wako sizikulakalaka china chilichonse koma phindu lachinyengo,+ anthu osalakwa kuti ukhetse magazi awo+ komanso kuba mwachinyengo ndi kulanda.’
17 ‘Ndithudi, maso ako ndi mtima wako sizikulakalaka china chilichonse koma phindu lachinyengo,+ anthu osalakwa kuti ukhetse magazi awo+ komanso kuba mwachinyengo ndi kulanda.’