Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 9:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Pambuyo pake, mfumu Yehoramu+ inabwerera ku Yezereeli+ kukachira zilonda zake zimene Asiriya anaivulaza pamene inali kumenyana ndi Hazaeli mfumu ya Siriya.+

      Kenako Yehu anati: “Ngati mukugwirizana nazo,+ musalole aliyense kuthawa kutuluka mumzinda uno kuti akanene ku Yezereeli.”

  • 2 Mbiri 22:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Anatsatira malangizo+ awo ndipo anapita kunkhondo ndi Yehoramu+ mwana wa Ahabu mfumu ya Isiraeli, kukamenyana ndi Hazaeli+ mfumu ya Siriya ku Ramoti-giliyadi.+ Kumeneko oponya mivi analasa Yehoramu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena