Numeri 28:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “‘M’mwezi woyamba, pa tsiku la 14, pazikhala pasika wa Yehova.+ Deuteronomo 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma uzipereka nsembe ya pasikayo pamalo amene Yehova Mulungu wako adzasankhe kuikapo dzina lake.+ Uzipereka nsembeyo madzulo, dzuwa likangolowa,+ pa nthawi yofanana ndi imene unatuluka mu Iguputo.
6 Koma uzipereka nsembe ya pasikayo pamalo amene Yehova Mulungu wako adzasankhe kuikapo dzina lake.+ Uzipereka nsembeyo madzulo, dzuwa likangolowa,+ pa nthawi yofanana ndi imene unatuluka mu Iguputo.