Deuteronomo 16:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Uzipereka nsembe ya pasika kwa Yehova Mulungu wako.+ Uzipereka nkhosa ndi ng’ombe+ pamalo amene Yehova adzasankhe kuikapo dzina lake.+
2 Uzipereka nsembe ya pasika kwa Yehova Mulungu wako.+ Uzipereka nkhosa ndi ng’ombe+ pamalo amene Yehova adzasankhe kuikapo dzina lake.+