Mateyu 26:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pa tsiku loyamba la chikondwerero cha mikate yopanda chofufumitsa,+ ophunzira anabwera kwa Yesu ndi kumufunsa kuti: “Kodi mukufuna tikakukonzereni kuti malo odyerako pasika?”+ Luka 22:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tsopano tsiku la chikondwerero cha mikate yopanda chofufumitsa linafika, tsiku loyenera kupha nyama yoperekera nsembe ya pasika.+
17 Pa tsiku loyamba la chikondwerero cha mikate yopanda chofufumitsa,+ ophunzira anabwera kwa Yesu ndi kumufunsa kuti: “Kodi mukufuna tikakukonzereni kuti malo odyerako pasika?”+
7 Tsopano tsiku la chikondwerero cha mikate yopanda chofufumitsa linafika, tsiku loyenera kupha nyama yoperekera nsembe ya pasika.+