Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 12:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “‘Tsiku limeneli lidzakhala chikumbutso kwa inu, ndipo muzichitira Yehova chikondwerero m’mibadwo yanu yonse. Limeneli ndi lamulo mpaka kalekale, kuti muzichita chikondwerero chimenechi.

  • Ekisodo 12:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 M’mwezi woyamba, tsiku la 14 la mwezi umenewo, madzulo muzidzadya mikate yopanda chofufumitsa, mpaka kukafika madzulo a tsiku la 21 mwezi womwewo.+

  • Levitiko 23:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “‘Pa tsiku la 15 m’mwezi umenewu, muzichita chikondwerero cha Yehova cha mikate yopanda chofufumitsa.+ Muzidya mikate yopanda chofufumitsa imeneyi masiku 7.+

  • Deuteronomo 16:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Uzipereka nsembe ya pasika kwa Yehova Mulungu wako.+ Uzipereka nkhosa ndi ng’ombe+ pamalo amene Yehova adzasankhe kuikapo dzina lake.+

  • Mateyu 26:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Pa tsiku loyamba la chikondwerero cha mikate yopanda chofufumitsa,+ ophunzira anabwera kwa Yesu ndi kumufunsa kuti: “Kodi mukufuna tikakukonzereni kuti malo odyerako pasika?”+

  • Maliko 14:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Tsopano pa tsiku loyamba la chikondwerero cha mikate yopanda chofufumitsa,+ pamene mwa mwambo anali kupereka nsembe nyama ya pasika, ophunzira ake+ anamufunsa kuti: “Kodi mukufuna tipite kuti kumene tikakukonzereni malo odyerako pasika?”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena