Levitiko 23:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 M’mwezi woyamba,* pa tsiku la 14 m’mweziwo,+ madzulo kuli kachisisira,* lizikhala tsiku la pasika+ wa Yehova. Levitiko 23:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “‘Pa tsiku la 15 m’mwezi umenewu, muzichita chikondwerero cha Yehova cha mikate yopanda chofufumitsa.+ Muzidya mikate yopanda chofufumitsa imeneyi masiku 7.+ Ezekieli 45:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “‘M’mwezi woyamba, pa tsiku la 14 la mweziwo, muzichita pasika.+ Muzichita chikondwerero chimenechi kwa masiku 7 ndipo muzidya mikate yopanda chofufumitsa.+
5 M’mwezi woyamba,* pa tsiku la 14 m’mweziwo,+ madzulo kuli kachisisira,* lizikhala tsiku la pasika+ wa Yehova.
6 “‘Pa tsiku la 15 m’mwezi umenewu, muzichita chikondwerero cha Yehova cha mikate yopanda chofufumitsa.+ Muzidya mikate yopanda chofufumitsa imeneyi masiku 7.+
21 “‘M’mwezi woyamba, pa tsiku la 14 la mweziwo, muzichita pasika.+ Muzichita chikondwerero chimenechi kwa masiku 7 ndipo muzidya mikate yopanda chofufumitsa.+